Yoswa 13:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 dziko la Agebala+ ndiponso dziko lonse la Lebanoni, kotulukira dzuwa, kuyambira ku Baala-gadi+ m’munsi mwa phiri la Herimoni mpaka kumalire ndi Hamati.+ Salimo 83:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Agebala, Aamoni,+ Aamaleki,Afilisiti+ pamodzi ndi anthu a ku Turo.+
5 dziko la Agebala+ ndiponso dziko lonse la Lebanoni, kotulukira dzuwa, kuyambira ku Baala-gadi+ m’munsi mwa phiri la Herimoni mpaka kumalire ndi Hamati.+