Oweruza 11:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Iye anakantha ana a Amoni kuyambira ku Aroweli mpaka kukafika ku Miniti,+ mizinda 20. Anawakantha koopsa mpaka kukafika ku Abele-kerami. Choncho ana a Amoni anagonja pamaso pa ana a Isiraeli.
33 Iye anakantha ana a Amoni kuyambira ku Aroweli mpaka kukafika ku Miniti,+ mizinda 20. Anawakantha koopsa mpaka kukafika ku Abele-kerami. Choncho ana a Amoni anagonja pamaso pa ana a Isiraeli.