Genesis 25:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Yokesani anabereka Sheba+ ndi Dedani.+ Ana a Dedani anali Asurimu, Letusimu ndi Leumimu.