2 Mafumu 17:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Anang’amba Isiraeli kumuchotsa kunyumba ya Davide ndipo iwo analonga ufumu Yerobowamu mwana wa Nebati.+ Yerobowamuyo anasiyitsa Aisiraeli kutsatira Yehova n’kuwachimwitsa ndi tchimo lalikulu.+
21 Anang’amba Isiraeli kumuchotsa kunyumba ya Davide ndipo iwo analonga ufumu Yerobowamu mwana wa Nebati.+ Yerobowamuyo anasiyitsa Aisiraeli kutsatira Yehova n’kuwachimwitsa ndi tchimo lalikulu.+