Yeremiya 18:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Choncho dziko lawo lidzakhala chinthu chodabwitsa kwa ena,+ chinthu chimene adzachiimbira mluzu mpaka kalekale.+ Aliyense wodutsa pafupi ndi dzikoli adzaliyang’anitsitsa modabwa ndipo adzapukusa mutu wake.+ Yeremiya 19:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndidzasandutsa mzindawu kukhala chinthu chodabwitsa kwa ena, chimene azidzachiimbira mluzu.+ Aliyense wodutsa pafupi nawo adzauyang’anitsitsa modabwa ndipo adzaulizira mluzu chifukwa cha miliri yake yonse.+ Chivumbulutso 18:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 “Amalonda oyendayenda+ a zinthu zimenezi, amene analemerera pa iye, adzaima patali chifukwa cha mantha poona kuzunzika kwake. Iwo adzamulira maliro ndi kumva chisoni+
16 Choncho dziko lawo lidzakhala chinthu chodabwitsa kwa ena,+ chinthu chimene adzachiimbira mluzu mpaka kalekale.+ Aliyense wodutsa pafupi ndi dzikoli adzaliyang’anitsitsa modabwa ndipo adzapukusa mutu wake.+
8 Ndidzasandutsa mzindawu kukhala chinthu chodabwitsa kwa ena, chimene azidzachiimbira mluzu.+ Aliyense wodutsa pafupi nawo adzauyang’anitsitsa modabwa ndipo adzaulizira mluzu chifukwa cha miliri yake yonse.+
15 “Amalonda oyendayenda+ a zinthu zimenezi, amene analemerera pa iye, adzaima patali chifukwa cha mantha poona kuzunzika kwake. Iwo adzamulira maliro ndi kumva chisoni+