Ezekieli 27:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Madera ako ali mkatikati mwa nyanja.+ Omwe anakupanga anakukongoletsa kwambiri.+