Genesis 25:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Pamenepo Yakobo anapatsa Esau mkate ndi mphodza, ndipo iye anadya n’kumwa.+ Kenako, ananyamuka n’kumapita. Umu ndi mmene Esau ananyozera ukulu wake.+
34 Pamenepo Yakobo anapatsa Esau mkate ndi mphodza, ndipo iye anadya n’kumwa.+ Kenako, ananyamuka n’kumapita. Umu ndi mmene Esau ananyozera ukulu wake.+