Yeremiya 23:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Koma adzalumbira kuti, ‘Pali Yehova Mulungu wamoyo amene anatulutsa a m’nyumba ya Isiraeli ndi kuwabweretsa kuno kuchokera m’dziko la kumpoto komanso kuchokera m’mayiko onse kumene ndinawabalalitsira’ ndipo adzakhala m’dziko lawo.”+ Ezekieli 36:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Inu mudzakhala m’dziko limene ndinapatsa makolo anu.+ Mudzakhala anthu anga ndipo ine ndidzakhala Mulungu wanu.’+
8 Koma adzalumbira kuti, ‘Pali Yehova Mulungu wamoyo amene anatulutsa a m’nyumba ya Isiraeli ndi kuwabweretsa kuno kuchokera m’dziko la kumpoto komanso kuchokera m’mayiko onse kumene ndinawabalalitsira’ ndipo adzakhala m’dziko lawo.”+
28 Inu mudzakhala m’dziko limene ndinapatsa makolo anu.+ Mudzakhala anthu anga ndipo ine ndidzakhala Mulungu wanu.’+