Yoweli 2:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Lizani lipenga m’Ziyoni+ amuna inu ndipo fuulani mfuu yankhondo+ m’phiri langa loyera.+ Anthu onse okhala m’dzikoli anjenjemere,+ pakuti tsiku la Yehova likubwera+ ndipo lili pafupi! Obadiya 15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Tsiku la Yehova limene adzawononge mitundu yonse ya anthu lili pafupi.+ Iwe adzakuchitira zofanana ndi zimene wachitira m’bale wako.+ Zimene unachita zidzabwerera pamutu pako.+ Zefaniya 1:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Khalani chete pamaso pa Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa,+ pakuti tsiku la Yehova lili pafupi,+ ndipo Yehova wakonza nsembe+ moti wakonzekeretsa*+ anthu amene wawaitana.
2 “Lizani lipenga m’Ziyoni+ amuna inu ndipo fuulani mfuu yankhondo+ m’phiri langa loyera.+ Anthu onse okhala m’dzikoli anjenjemere,+ pakuti tsiku la Yehova likubwera+ ndipo lili pafupi!
15 Tsiku la Yehova limene adzawononge mitundu yonse ya anthu lili pafupi.+ Iwe adzakuchitira zofanana ndi zimene wachitira m’bale wako.+ Zimene unachita zidzabwerera pamutu pako.+
7 Khalani chete pamaso pa Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa,+ pakuti tsiku la Yehova lili pafupi,+ ndipo Yehova wakonza nsembe+ moti wakonzekeretsa*+ anthu amene wawaitana.