Danieli 4:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Mtengowo ndinuyo mfumu,+ chifukwa mwakula ndipo mwakhala ndi mphamvu. Ulemerero wanu wakula mpaka kufika kumwamba+ ndipo ulamuliro wanu wafika kumalekezero a dziko lapansi.+ Amosi 2:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 “‘Koma ine ndinawononga Aamori+ chifukwa cha anthu anga. Aamoriwo misinkhu yawo inali yofanana ndi mitengo ya mkungudza ndipo mphamvu zawo zinali zofanana ndi za mitengo ikuluikulu.+ Ndinawononga zipatso zawo m’mwamba ndiponso mizu yawo pansi.+
22 Mtengowo ndinuyo mfumu,+ chifukwa mwakula ndipo mwakhala ndi mphamvu. Ulemerero wanu wakula mpaka kufika kumwamba+ ndipo ulamuliro wanu wafika kumalekezero a dziko lapansi.+
9 “‘Koma ine ndinawononga Aamori+ chifukwa cha anthu anga. Aamoriwo misinkhu yawo inali yofanana ndi mitengo ya mkungudza ndipo mphamvu zawo zinali zofanana ndi za mitengo ikuluikulu.+ Ndinawononga zipatso zawo m’mwamba ndiponso mizu yawo pansi.+