Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Maliro 4:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Wodzozedwa wa Yehova,+ amene ndi mpweya wotuluka mphuno mwathu,+ wagwidwa m’dzenje lawo lalikulu.+

      Ponena za ameneyu, ife tinati: “Tidzakhala mumthunzi wake+ pakati pa mitundu ya anthu.”+

  • Ezekieli 30:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 “Yehova wanena kuti, ‘Nawonso othandiza Iguputo adzaphedwa, ndipo mphamvu zimene amazinyadira zidzatha.’+

      “‘Kuchokera ku Migidoli+ mpaka ku Seyene,+ anthu adzaphedwa ndi lupanga m’dzikolo,’ watero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.

  • Ezekieli 32:31
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 31 “‘Amenewa ndiwo anthu amene Farao adzawaone ndipo mtima wake udzakhala pansi poona khamu lake lonse.+ Farao ndi gulu lake lonse lankhondo adzakhala m’gulu la anthu ophedwa ndi lupanga,’ watero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena