Ezekieli 27:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Anthu onse okhala m’zilumba+ adzakuyang’anitsitsa modabwa ndipo mafumu awo adzanjenjemera chifukwa cha mantha.+ Nkhope zawo zonse zidzaoneka zankhawa.+
35 Anthu onse okhala m’zilumba+ adzakuyang’anitsitsa modabwa ndipo mafumu awo adzanjenjemera chifukwa cha mantha.+ Nkhope zawo zonse zidzaoneka zankhawa.+