Genesis 10:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Kanani anabereka Sidoni+ mwana wake woyamba, kenako anabereka Heti.+ Ezekieli 28:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 “Iwe mwana wa munthu, yang’ana ku Sidoni+ ndipo ulosere zoipa zimene zidzamuchitikire.