Salimo 130:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Isiraeli ayembekezere Yehova,+Pakuti Yehova amasonyeza kukoma mtima kosatha.+Iye ali ndi mphamvu zochuluka zowombolera anthu ake.+
7 Isiraeli ayembekezere Yehova,+Pakuti Yehova amasonyeza kukoma mtima kosatha.+Iye ali ndi mphamvu zochuluka zowombolera anthu ake.+