Yakobo 1:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Komabe muzichita zimene mawu amanena,+ osati kungomva chabe, n’kumadzinyenga ndi maganizo onama.+