Yeremiya 21:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ndidzamenyana nanu+ ndi mkono wotambasula ndiponso dzanja lamphamvu. Ndidzachita zimenezi nditakwiya, nditapsa mtima, ndiponso ndili ndi ukali waukulu.+ Ezekieli 15:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Anthuwo ndawayang’ana mokwiya.+ Iwo achoka pamoto, koma motowo uwanyeketsa.+ Anthu inu mudzadziwa kuti ine ndine Yehova, ndikadzawayang’ana mokwiya.’”+
5 Ndidzamenyana nanu+ ndi mkono wotambasula ndiponso dzanja lamphamvu. Ndidzachita zimenezi nditakwiya, nditapsa mtima, ndiponso ndili ndi ukali waukulu.+
7 Anthuwo ndawayang’ana mokwiya.+ Iwo achoka pamoto, koma motowo uwanyeketsa.+ Anthu inu mudzadziwa kuti ine ndine Yehova, ndikadzawayang’ana mokwiya.’”+