Salimo 23:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Yehova ndi M’busa wanga.+Sindidzasowa kanthu.+ Yeremiya 3:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ndidzakupatsani abusa amene mtima wanga wakonda+ ndipo iwo adzakuthandizani kudziwa zinthu zambiri ndiponso kumvetsa bwino zinthu.+
15 Ndidzakupatsani abusa amene mtima wanga wakonda+ ndipo iwo adzakuthandizani kudziwa zinthu zambiri ndiponso kumvetsa bwino zinthu.+