Zefaniya 3:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Otsala mwa Isiraeli+ sadzachita zinthu zosalungama+ kapena kunena bodza.+ Sadzakhala ndi lilime lachinyengo+ koma iwo adzadya ndi kugona pansi momasuka+ ndipo sipadzakhala wowaopsa.”+
13 Otsala mwa Isiraeli+ sadzachita zinthu zosalungama+ kapena kunena bodza.+ Sadzakhala ndi lilime lachinyengo+ koma iwo adzadya ndi kugona pansi momasuka+ ndipo sipadzakhala wowaopsa.”+