Mika 4:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Yehova wanena kuti, “Pa tsiku limenelo, ndidzasonkhanitsa anthu amene anali kuyenda motsimphina.+ Anthu amene anamwazikana ndidzawasonkhanitsa pamodzi.+ Ndidzasonkhanitsa pamodzi anthu amene ndawasautsa. Mateyu 15:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Poyankha iye anati: “Ine sananditumize kwa wina aliyense koma kwa nkhosa zotayika za nyumba ya Isiraeli.”+ Luka 15:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 “Ndani wa inu amene atakhala ndi nkhosa 100, imodzi n’kutayika, sangasiye nkhosa 99 zinazo m’chipululu, n’kupita kukafunafuna imodzi yotayikayo kufikira ataipeza?+
6 Yehova wanena kuti, “Pa tsiku limenelo, ndidzasonkhanitsa anthu amene anali kuyenda motsimphina.+ Anthu amene anamwazikana ndidzawasonkhanitsa pamodzi.+ Ndidzasonkhanitsa pamodzi anthu amene ndawasautsa.
24 Poyankha iye anati: “Ine sananditumize kwa wina aliyense koma kwa nkhosa zotayika za nyumba ya Isiraeli.”+
4 “Ndani wa inu amene atakhala ndi nkhosa 100, imodzi n’kutayika, sangasiye nkhosa 99 zinazo m’chipululu, n’kupita kukafunafuna imodzi yotayikayo kufikira ataipeza?+