Salimo 109:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Chifukwa chakuti sanakumbukire kusonyeza kukoma mtima kosatha,+M’malomwake anapitiriza kuthamangitsa wosautsika ndi wosauka,+Komanso munthu wa mtima wachisoni kuti amuphe.+ Obadiya 15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Tsiku la Yehova limene adzawononge mitundu yonse ya anthu lili pafupi.+ Iwe adzakuchitira zofanana ndi zimene wachitira m’bale wako.+ Zimene unachita zidzabwerera pamutu pako.+ Aroma 2:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Iye adzaweruza aliyense malinga ndi ntchito zake motere:+ Agalatiya 6:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Musanyengedwe,+ Mulungu sapusitsika.+ Chilichonse chimene munthu wafesa, adzakololanso chomwecho.+
16 Chifukwa chakuti sanakumbukire kusonyeza kukoma mtima kosatha,+M’malomwake anapitiriza kuthamangitsa wosautsika ndi wosauka,+Komanso munthu wa mtima wachisoni kuti amuphe.+
15 Tsiku la Yehova limene adzawononge mitundu yonse ya anthu lili pafupi.+ Iwe adzakuchitira zofanana ndi zimene wachitira m’bale wako.+ Zimene unachita zidzabwerera pamutu pako.+