Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 109:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Iye anakonda kutemberera ena,+ mwakuti matemberero anabwera kwa iye.+

      Koma kudalitsa ena sikunali kumusangalatsa,+

      Moti madalitso anali patali ndi iye,+

  • Ezekieli 25:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 ‘Ine ndidzalanga Edomu kudzera mwa anthu anga Aisiraeli.+ Aisiraeliwo adzachitira Edomu mogwirizana ndi mkwiyo komanso ukali wanga, ndipo Aedomuwo adzadziwa mmene ndimalangira,’+ watero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.”’

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena