Oweruza 5:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 M’masiku a Samagara+ mwana wa Anati,M’masiku a Yaeli,+ m’njira munalibe odutsamo,Ndipo oyenda m’misewu anayamba kuyenda njira zolambalala.+ Ezekieli 29:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 M’dziko lako simudzaponda phazi la munthu+ kapena la chiweto,+ ndipo simudzakhala munthu aliyense kwa zaka 40.+
6 M’masiku a Samagara+ mwana wa Anati,M’masiku a Yaeli,+ m’njira munalibe odutsamo,Ndipo oyenda m’misewu anayamba kuyenda njira zolambalala.+
11 M’dziko lako simudzaponda phazi la munthu+ kapena la chiweto,+ ndipo simudzakhala munthu aliyense kwa zaka 40.+