Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yeremiya 49:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 “Edomu adzakhala chinthu chodabwitsa.+ Aliyense wodutsa pafupi naye adzamuyang’anitsitsa modabwa ndi kumuimbira mluzu chifukwa cha miliri yonse imene idzamugwera.+

  • Yeremiya 49:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Monga mmene Sodomu ndi Gomora pamodzi ndi midzi yapafupi inawonongedwera,+ Edomu adzawonongedwanso moti palibe munthu amene adzakhalanso m’dzikolo. Mwana wa munthu sadzakhalanso mmenemo ngati mlendo,”+ watero Yehova.

  • Ezekieli 25:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: “Ine ndidzatambasulira Edomu+ dzanja langa ndi kupha anthu ndi ziweto m’dzikolo.+ Ndidzalisandutsa bwinja kuyambira ku Temani+ mpaka ku Dedani.+ Iwo adzaphedwa ndi lupanga.

  • Malaki 1:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 “Popeza kuti Edomu akunena kuti, ‘Ife tawonongedwa, koma tibwerera ndi kukamanga malo athu owonongedwawo,’ Yehova wa makamu wanena kuti, ‘Iwo akamanga, koma ine ndikagwetsa.+ Anthu adzatcha malo awowo, “dera la zoipa” ndipo iwowo adzatchedwa, “anthu okanidwa ndi Yehova+ mpaka kalekale.”*

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena