Zekariya 8:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 “Yehova wa makamu wanena kuti, ‘M’bwalo la mzinda wa Yerusalemu mudzakhala amuna ndi akazi achikulire.+ Aliyense adzatenga ndodo+ m’dzanja lake pakuti masiku ake adzakhala atachuluka.
4 “Yehova wa makamu wanena kuti, ‘M’bwalo la mzinda wa Yerusalemu mudzakhala amuna ndi akazi achikulire.+ Aliyense adzatenga ndodo+ m’dzanja lake pakuti masiku ake adzakhala atachuluka.