Hoseya 2:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Ndidzalonjeza kukukwatira mokhulupirika ndipo udzadziwadi Yehova.’+ Yoweli 3:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Pamenepo anthu inu mudzadziwa kuti ine ndine Yehova Mulungu wanu,+ amene ndimakhala mu Ziyoni, phiri langa lopatulika.+ Yerusalemu adzakhala malo anga opatulika,+ ndipo alendo sadzadutsanso mmenemo.+
17 Pamenepo anthu inu mudzadziwa kuti ine ndine Yehova Mulungu wanu,+ amene ndimakhala mu Ziyoni, phiri langa lopatulika.+ Yerusalemu adzakhala malo anga opatulika,+ ndipo alendo sadzadutsanso mmenemo.+