Yeremiya 15:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndipeta anthu anga ngati mbewu kuzipata za m’dzikoli. Ndithu, ndiwauluza ndi chifoloko.+ Ndiwaphera ana awo+ ndipo ndiwononga anthu anga chifukwa sanasiye kuchita zinthu zoipa.+
7 Ndipeta anthu anga ngati mbewu kuzipata za m’dzikoli. Ndithu, ndiwauluza ndi chifoloko.+ Ndiwaphera ana awo+ ndipo ndiwononga anthu anga chifukwa sanasiye kuchita zinthu zoipa.+