Ezekieli 23:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Iwo achita chigololo+ ndipo m’manja mwawo muli magazi.+ Achita chigololo ndi mafano awo onyansa.+ Kuwonjezera apo, ana anga aamuna amene anandiberekera anawaponya pamoto kuti akhale chakudya cha mafanowo.+
37 Iwo achita chigololo+ ndipo m’manja mwawo muli magazi.+ Achita chigololo ndi mafano awo onyansa.+ Kuwonjezera apo, ana anga aamuna amene anandiberekera anawaponya pamoto kuti akhale chakudya cha mafanowo.+