Zekariya 8:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndithu ndidzawabweretsa, ndipo adzakhala mu Yerusalemu.+ Iwo adzakhala anthu anga+ ndipo ine ndidzakhala Mulungu wawo woona ndi wachilungamo.’”+
8 Ndithu ndidzawabweretsa, ndipo adzakhala mu Yerusalemu.+ Iwo adzakhala anthu anga+ ndipo ine ndidzakhala Mulungu wawo woona ndi wachilungamo.’”+