Ezekieli 17:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Mitengo yonse yamthengo idzadziwa kuti ine Yehova+ ndatsitsa mtengo waukulu+ ndi kukweza mtengo wonyozeka,+ ndaumitsa mtengo wauwisi+ ndi kuchititsa maluwa mtengo umene unali wouma. Ine Yehova ndanena ndi kuchita zimenezi.”’”+ Ezekieli 37:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Malo anga opatulika akadzakhala pakati pawo mpaka kalekale, mitundu ina ya anthu idzadziwa kuti ine Yehova+ ndikuyeretsa Isiraeli.”’”+
24 Mitengo yonse yamthengo idzadziwa kuti ine Yehova+ ndatsitsa mtengo waukulu+ ndi kukweza mtengo wonyozeka,+ ndaumitsa mtengo wauwisi+ ndi kuchititsa maluwa mtengo umene unali wouma. Ine Yehova ndanena ndi kuchita zimenezi.”’”+
28 Malo anga opatulika akadzakhala pakati pawo mpaka kalekale, mitundu ina ya anthu idzadziwa kuti ine Yehova+ ndikuyeretsa Isiraeli.”’”+