Ekisodo 23:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Katatu pa chaka mwamuna aliyense pakati panu azionekera pamaso pa Ambuye woona, Yehova.+ 2 Mbiri 7:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Pa nthawi imeneyo Solomo anachita chikondwerero+ masiku 7 pamodzi ndi Aisiraeli onse.+ Unali mpingo waukulu+ wa anthu amene anachokera kumadera osiyanasiyana, kuyambira polowera ku Hamati+ n’kutsetsereka mpaka kukafika kuchigwa* cha Iguputo.+
8 Pa nthawi imeneyo Solomo anachita chikondwerero+ masiku 7 pamodzi ndi Aisiraeli onse.+ Unali mpingo waukulu+ wa anthu amene anachokera kumadera osiyanasiyana, kuyambira polowera ku Hamati+ n’kutsetsereka mpaka kukafika kuchigwa* cha Iguputo.+