Ezekieli 1:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Yehova analankhula+ ndi Ezekieli,+ mwana wa wansembe Buzi, pamene anali m’dziko la Akasidi+ pafupi ndi mtsinje wa Kebara. Dzanja la Yehova linafika pa iye kumeneko.+
3 Yehova analankhula+ ndi Ezekieli,+ mwana wa wansembe Buzi, pamene anali m’dziko la Akasidi+ pafupi ndi mtsinje wa Kebara. Dzanja la Yehova linafika pa iye kumeneko.+