Yesaya 32:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 kufikira mzimu utatsanulidwa pa ife kuchokera kumwamba,+ ndiponso chipululu chitakhala munda wa zipatso. Munda wa zipatsowo udzakhala ngati nkhalango yeniyeni.+ Ezekieli 36:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Ndidzaika mzimu wanga mwa inu,+ ndipo ndidzakuchititsani kuyenda motsatira malamulo anga.+ Mudzasunga zigamulo zanga ndi kuzitsatira.+ Ezekieli 37:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 “‘Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wauza mafupa awa kuti: “Ndiika mpweya mwa inu ndipo mukhala amoyo.+
15 kufikira mzimu utatsanulidwa pa ife kuchokera kumwamba,+ ndiponso chipululu chitakhala munda wa zipatso. Munda wa zipatsowo udzakhala ngati nkhalango yeniyeni.+
27 Ndidzaika mzimu wanga mwa inu,+ ndipo ndidzakuchititsani kuyenda motsatira malamulo anga.+ Mudzasunga zigamulo zanga ndi kuzitsatira.+
5 “‘Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wauza mafupa awa kuti: “Ndiika mpweya mwa inu ndipo mukhala amoyo.+