Ezekieli 34:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Ine Yehova ndidzakhala Mulungu wawo,+ ndipo mtumiki wanga Davide adzakhala mtsogoleri pakati pawo.+ Ine Yehova ndanena zimenezi. Luka 1:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Ameneyu adzakhala wamkulu+ ndipo adzatchedwa Mwana wa Wam’mwambamwamba.+ Yehova Mulungu adzam’patsa mpando wachifumu+ wa Davide atate wake.+ Yohane 12:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Pamenepo khamu la anthulo linamuyankha kuti: “Ife tinamva m’Chilamulo kuti Khristu adzakhala kosatha.+ Nanga inu mukunena bwanji kuti Mwana wa munthu adzakwezedwa m’mwamba?+ Kodi Mwana wa munthu ameneyo ndani?”+
24 Ine Yehova ndidzakhala Mulungu wawo,+ ndipo mtumiki wanga Davide adzakhala mtsogoleri pakati pawo.+ Ine Yehova ndanena zimenezi.
32 Ameneyu adzakhala wamkulu+ ndipo adzatchedwa Mwana wa Wam’mwambamwamba.+ Yehova Mulungu adzam’patsa mpando wachifumu+ wa Davide atate wake.+
34 Pamenepo khamu la anthulo linamuyankha kuti: “Ife tinamva m’Chilamulo kuti Khristu adzakhala kosatha.+ Nanga inu mukunena bwanji kuti Mwana wa munthu adzakwezedwa m’mwamba?+ Kodi Mwana wa munthu ameneyo ndani?”+