Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 7:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Komabe Farao sadzakumverani,+ motero ndidzaonetsa mphamvu ya dzanja langa pa Iguputo ndi kutulutsa makamu anga,+ anthu anga,+ ana a Isiraeli,+ m’dziko la Iguputo ndi ziweruzo zamphamvu.+

  • Ekisodo 8:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Ataona zimenezi ansembe ochita zamatsenga anauza Farao kuti: “Chimenechi ndi chala cha Mulungu!”+ Koma Farao anapitiriza kuumitsa mtima wake,+ ndipo sanamvere, monga momwe Yehova ananenera.

  • 1 Samueli 5:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Anthu a ku Asidodi ataona kuti zafika pamenepo, anati: “Musalole kuti likasa la Mulungu wa Isiraeli likhale ndi ife kuno, chifukwa dzanja lake latisautsa kwambiri pamodzi ndi Dagoni mulungu wathu.”+

  • 1 Samueli 6:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Ndiyeno muonetsetse izi: Likasalo likadzalowera njira yopita kwawo, ku Beti-semesi,+ ndiye kuti iye ndi amenedi watichitira choipa chachikuluchi. Koma ngati sililowera kumeneko, tidziwa kuti si dzanja lake limene latikhudza, koma ngozi+ yangotigwera.”

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena