Ezekieli 1:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Mapazi awo anali owongoka, ndipo kupansi kwa mapazi awo kunali ngati kupansi kwa mapazi a mwana wa ng’ombe.+ Mapaziwo anali kuwala ngati mkuwa wopukutidwa bwino.+ Danieli 10:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Thupi lake linali ngati mwala wa kulusolito,+ nkhope yake inali yowala ngati mphezi,+ maso ake anali kuoneka ngati miyuni yamoto,+ manja ake ndi mapazi ake zinali kuoneka ngati mkuwa wonyezimira,+ ndipo mawu ake anali kumveka ngati khamu la anthu.
7 Mapazi awo anali owongoka, ndipo kupansi kwa mapazi awo kunali ngati kupansi kwa mapazi a mwana wa ng’ombe.+ Mapaziwo anali kuwala ngati mkuwa wopukutidwa bwino.+
6 Thupi lake linali ngati mwala wa kulusolito,+ nkhope yake inali yowala ngati mphezi,+ maso ake anali kuoneka ngati miyuni yamoto,+ manja ake ndi mapazi ake zinali kuoneka ngati mkuwa wonyezimira,+ ndipo mawu ake anali kumveka ngati khamu la anthu.