Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Levitiko 8:35
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 35 Chotero mukhale pakhomo la chihema chokumanako usana ndi usiku kwa masiku 7.+ Ndipo muyenera kuchita ulonda umene Yehova walamula,+ kuti musafe. Chifukwa n’zimene ndalamulidwa.”

  • Numeri 3:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Iwo ayenera kutumikira iye ndi kutumikiranso khamu lonse pa ntchito za pachihema chokumanako.

  • Numeri 3:32
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 32 Mkulu wa atsogoleri onse a Alevi anali Eleazara,+ mwana wa wansembe Aroni. Iye ndiye anali kuyang’anira onse otumikira pamalo oyera.

  • 1 Mbiri 9:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Iwo ndi ana awo anali kuyang’anira zipata za nyumba ya Yehova, kapena kuti chihema chopatulika,* ndipo ankachita utumiki waulonda.+

  • 2 Mbiri 13:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Iwo akufukiza nsembe zopsereza kwa Yehova m’mawa uliwonse ndi madzulo alionse.+ Akufukizanso mafuta onunkhira+ ndipo mikate yosanjikiza ili patebulo la golide woyenga bwino.+ Tilinso ndi choikapo nyale chagolide+ ndi nyale zake zimene amayatsa madzulo alionse.+ Tikuchita zimenezi chifukwa tikukwaniritsa udindo wathu+ kwa Yehova Mulungu wathu, koma inuyo mwamusiya.+

  • Salimo 134:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 134 Tamandani Yehova,+

      Inu nonse atumiki a Yehova,+

      Inu amene mumaimirira m’nyumba ya Yehova usiku.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena