Levitiko 6:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ndipo moto wa paguwa lansembe uziyaka nthawi zonse. Usamazime. Wansembe aziponyapo nkhuni+ m’mawa uliwonse ndi kuikapo nsembe yopsereza pankhunipo. Akatero, azitentha mafuta a nsembe yachiyanjano pamotopo.+ Numeri 18:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Muzichita utumiki wanu m’malo oyera+ ndi paguwa lansembe,+ kuti mkwiyo+ usadzawabukirenso ana a Isiraeli.
12 Ndipo moto wa paguwa lansembe uziyaka nthawi zonse. Usamazime. Wansembe aziponyapo nkhuni+ m’mawa uliwonse ndi kuikapo nsembe yopsereza pankhunipo. Akatero, azitentha mafuta a nsembe yachiyanjano pamotopo.+
5 Muzichita utumiki wanu m’malo oyera+ ndi paguwa lansembe,+ kuti mkwiyo+ usadzawabukirenso ana a Isiraeli.