Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Mafumu 7:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Ndiyeno Hiramu anaika zipilala+ zija pakhonde+ la kachisi. Chipilala chimodzi anachiika mbali ya kudzanja lamanja n’kuchitcha Yakini. Chipilala china anachiika mbali ya kumanzere n’kuchitcha Boazi.

  • Yeremiya 52:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Zipilala zamkuwa+ zimene zinali panyumba ya Yehova, zotengera zokhala ndi mawilo+ ndi chosungiramo madzi chamkuwa+ zimene zinali m’nyumba ya Yehova, Akasidi anaziphwanyaphwanya n’kutenga mkuwa wakewo kupita nawo ku Babulo.+

  • Chivumbulutso 3:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 “‘Wopambana pa nkhondo, ndidzamuika kukhala mzati+ m’kachisi+ wa Mulungu wanga,+ ndipo sadzachokamonso. Ndidzamulemba dzina la Mulungu wanga, ndiponso dzina la mzinda wa Mulungu wanga, Yerusalemu watsopano,+ wotsika kuchokera kumwamba kwa Mulungu wanga. Ndidzamulembanso dzina langa latsopano.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena