Ezekieli 11:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 kuti azidzatsatira malamulo anga, azidzasunga zigamulo zanga ndi kuzikwaniritsa.+ Iwo adzakhaladi anthu anga+ ndipo ine ndidzakhala Mulungu wawo.”’+ Ezekieli 36:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Ndidzaika mzimu wanga mwa inu,+ ndipo ndidzakuchititsani kuyenda motsatira malamulo anga.+ Mudzasunga zigamulo zanga ndi kuzitsatira.+ Yohane 13:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ngati zimenezi mukuzidziwa, ndinu odala mukamazichita.+
20 kuti azidzatsatira malamulo anga, azidzasunga zigamulo zanga ndi kuzikwaniritsa.+ Iwo adzakhaladi anthu anga+ ndipo ine ndidzakhala Mulungu wawo.”’+
27 Ndidzaika mzimu wanga mwa inu,+ ndipo ndidzakuchititsani kuyenda motsatira malamulo anga.+ Mudzasunga zigamulo zanga ndi kuzitsatira.+