Levitiko 1:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 “‘Kenako azipha ng’ombe yaing’onoyo pamaso pa Yehova. Ndiyeno ana a Aroni, ansembe,+ azibweretsa magazi ake ndi kuwawaza mozungulira paguwa lansembe,+ limene lili pakhomo la chihema chokumanako. Levitiko 8:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Mose anapha nkhosayo ndi kuwaza magazi ake mozungulira paguwa lansembe.+ Ezekieli 45:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Wansembe azitenga ena mwa magazi a nsembe yamachimo ndi kuwapaka pafelemu+ la Nyumbayi ndi pamakona anayi a chigawo chachitatu cha guwa lansembe.+ Aziwapakanso pafelemu la kanyumba ka pachipata cha bwalo lamkati.
5 “‘Kenako azipha ng’ombe yaing’onoyo pamaso pa Yehova. Ndiyeno ana a Aroni, ansembe,+ azibweretsa magazi ake ndi kuwawaza mozungulira paguwa lansembe,+ limene lili pakhomo la chihema chokumanako.
19 Wansembe azitenga ena mwa magazi a nsembe yamachimo ndi kuwapaka pafelemu+ la Nyumbayi ndi pamakona anayi a chigawo chachitatu cha guwa lansembe.+ Aziwapakanso pafelemu la kanyumba ka pachipata cha bwalo lamkati.