Ekisodo 29:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Koma nyama ya ng’ombeyo, chikopa chake ndi ndowe zake uzitenthe ndi moto kunja kwa msasa.+ Ng’ombeyo ndi nsembe yamachimo. Levitiko 8:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Koma chikopa cha ng’ombeyo, nyama yake ndi ndowe zake anazitentha kunja kwa msasa,+ monga mmene Yehova analamulira Mose. Aheberi 13:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Pakuti nyama zimene magazi ake, mkulu wa ansembe amalowa nawo m’malo oyera chifukwa cha machimo, amakazitentha kunja kwa msasa.+
14 Koma nyama ya ng’ombeyo, chikopa chake ndi ndowe zake uzitenthe ndi moto kunja kwa msasa.+ Ng’ombeyo ndi nsembe yamachimo.
17 Koma chikopa cha ng’ombeyo, nyama yake ndi ndowe zake anazitentha kunja kwa msasa,+ monga mmene Yehova analamulira Mose.
11 Pakuti nyama zimene magazi ake, mkulu wa ansembe amalowa nawo m’malo oyera chifukwa cha machimo, amakazitentha kunja kwa msasa.+