Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 28:39
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 39 “Kenako uwombe mkanjo wamandalasi ndi ulusi wabwino kwambiri. Upangenso nduwira ya nsalu yabwino kwambiri,+ ndiponso uwombe lamba+ wa mkanjo.

  • Ekisodo 39:27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 Kenako anawomba mikanjo ya Aroni ndi ana ake ya ulusi wabwino kwambiri.+

  • Levitiko 16:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Azivala mkanjo wopatulika wowomba,+ kabudula wansalu+ wobisa thupi lake, lamba wansalu wa pamimba,+ ndipo azikulunga kumutu kwake ndi nduwira yansalu.+ Zimenezi ndi zovala zopatulika.+ Iye azivala zimenezi atasamba thupi lonse.+

  • Chivumbulutso 19:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Iye waloledwa kuvala zovala zapamwamba, zonyezimira ndi zoyera bwino, pakuti zovala zapamwambazo zikuimira ntchito zolungama za oyera.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena