1 Mbiri 23:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Pakati pawo panali oyang’anira ntchito ya panyumba ya Yehova okwana 24,000. Akapitawo+ ndi oweruza+ analipo 6,000. 2 Mbiri 19:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ku Yerusalemu nakonso Yehosafati anaikako Alevi ena,+ ansembe,+ ndi ena mwa atsogoleri a nyumba za makolo+ a Isiraeli, kuti azionetsetsa kuti anthu akutsatira chilamulo+ cha Yehova ndi kuti aziweruza milandu+ ya anthu a ku Yerusalemu.
4 Pakati pawo panali oyang’anira ntchito ya panyumba ya Yehova okwana 24,000. Akapitawo+ ndi oweruza+ analipo 6,000.
8 Ku Yerusalemu nakonso Yehosafati anaikako Alevi ena,+ ansembe,+ ndi ena mwa atsogoleri a nyumba za makolo+ a Isiraeli, kuti azionetsetsa kuti anthu akutsatira chilamulo+ cha Yehova ndi kuti aziweruza milandu+ ya anthu a ku Yerusalemu.