Levitiko 4:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 “‘Ngati wansembe, wodzozedwa,+ wachita tchimo+ limene lapalamulitsa anthu onse, azipereka kwa Yehova ng’ombe yaing’ono yamphongo yopanda chilema monga nsembe yamachimo chifukwa cha tchimo lakelo.+ Levitiko 8:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Atatero anabweretsa ng’ombe yamphongo+ ya nsembe yamachimo, ndipo Aroni ndi ana ake anaika manja awo pamutu+ pa ng’ombe ya nsembe yamachimoyo.
3 “‘Ngati wansembe, wodzozedwa,+ wachita tchimo+ limene lapalamulitsa anthu onse, azipereka kwa Yehova ng’ombe yaing’ono yamphongo yopanda chilema monga nsembe yamachimo chifukwa cha tchimo lakelo.+
14 Atatero anabweretsa ng’ombe yamphongo+ ya nsembe yamachimo, ndipo Aroni ndi ana ake anaika manja awo pamutu+ pa ng’ombe ya nsembe yamachimoyo.