Ekisodo 22:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 “Inuyo muzikhala anthu oyera pamaso panga+ ndipo musadye nyama imene yaphedwa ndi chilombo kuthengo.+ Imeneyo muziponyera agalu.+ Levitiko 22:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Iye asadye nyama iliyonse imene waipeza yakufa, kapena iliyonse yophedwa ndi zilombo, chifukwa angakhale wodetsedwa.+ Ine ndine Yehova. Deuteronomo 14:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 “Musadye nyama iliyonse imene mwaipeza yakufa.+ Muziipereka kwa mlendo wokhala mumzinda wanu kuti adye, kapena muziigulitsa kwa mlendo* chifukwa inu ndinu anthu oyera kwa Yehova Mulungu wanu. “Musawiritse mwana wa mbuzi mumkaka wa mayi wake.+
31 “Inuyo muzikhala anthu oyera pamaso panga+ ndipo musadye nyama imene yaphedwa ndi chilombo kuthengo.+ Imeneyo muziponyera agalu.+
8 Iye asadye nyama iliyonse imene waipeza yakufa, kapena iliyonse yophedwa ndi zilombo, chifukwa angakhale wodetsedwa.+ Ine ndine Yehova.
21 “Musadye nyama iliyonse imene mwaipeza yakufa.+ Muziipereka kwa mlendo wokhala mumzinda wanu kuti adye, kapena muziigulitsa kwa mlendo* chifukwa inu ndinu anthu oyera kwa Yehova Mulungu wanu. “Musawiritse mwana wa mbuzi mumkaka wa mayi wake.+