Yesaya 66:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 “Kuyambira mwezi watsopano mpaka mwezi wina watsopano, ndiponso sabata ndi sabata, anthu onse adzabwera kudzagwada pamaso panga,”+ watero Yehova. Luka 1:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Khamu lonse la anthu linali kupemphera panja, pa ola lopereka nsembe zofukizalo.+
23 “Kuyambira mwezi watsopano mpaka mwezi wina watsopano, ndiponso sabata ndi sabata, anthu onse adzabwera kudzagwada pamaso panga,”+ watero Yehova.