Amosi 8:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Inu mukunena kuti: ‘Kodi mwezi watsopano utha liti+ kuti tiyambe kugulitsa chakudya?*+ Komanso sabata+ litha liti kuti tiyambe kuchepetsa muyezo wogulitsira zinthu,+ kukweza mtengo ndi kubera wogula mwa kugwiritsa ntchito masikelo achinyengo?+
5 Inu mukunena kuti: ‘Kodi mwezi watsopano utha liti+ kuti tiyambe kugulitsa chakudya?*+ Komanso sabata+ litha liti kuti tiyambe kuchepetsa muyezo wogulitsira zinthu,+ kukweza mtengo ndi kubera wogula mwa kugwiritsa ntchito masikelo achinyengo?+