-
Ezekieli 45:17Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
17 Mtsogoleri+ wa anthu adzapatsidwa udindo woyang’anira nsembe zopsereza zathunthu,+ nsembe yambewu+ ndi nsembe yachakumwa.+ Iye azidzayang’anira nsembezo pa nthawi ya zikondwerero,+ pa masiku okhala mwezi,+ pa nthawi ya masabata+ ndi pa nthawi ya zikondwerero zonse za nyumba ya Isiraeli.+ Mtsogoleriyo ndi amene azidzapereka kwa ansembe nyama za nsembe yamachimo, nsembe yambewu, nsembe yopsereza yathunthu ndi nsembe zachiyanjano kuti aphimbe machimo a nyumba ya Isiraeli.’
-