Aheberi 10:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Pakuti ngati tikuchita machimo mwadala+ pambuyo podziwa choonadi molondola,+ palibe nsembe ina yotsala imene ingaperekedwe chifukwa cha machimo athuwo.+ Chivumbulutso 22:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Amene akuchita zosalungama, achitebe zosalungama,+ ndipo wochita zonyansa apitirizebe kuchita zonyansazo.+ Koma wolungama+ achitebe chilungamo, ndipo woyera apitirizebe kuyeretsedwa.+
26 Pakuti ngati tikuchita machimo mwadala+ pambuyo podziwa choonadi molondola,+ palibe nsembe ina yotsala imene ingaperekedwe chifukwa cha machimo athuwo.+
11 Amene akuchita zosalungama, achitebe zosalungama,+ ndipo wochita zonyansa apitirizebe kuchita zonyansazo.+ Koma wolungama+ achitebe chilungamo, ndipo woyera apitirizebe kuyeretsedwa.+