Ezekieli 47:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Nditatuluka m’madzimo ndinangoona kuti m’mphepete mwa mtsinjewo munali mitengo yambirimbiri kumbali iyi ndi kumbali inayo.+
7 Nditatuluka m’madzimo ndinangoona kuti m’mphepete mwa mtsinjewo munali mitengo yambirimbiri kumbali iyi ndi kumbali inayo.+